2 Samueli 18:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndiyeno Yowabu anauza Mkusi+ kuti: “Pita ukauze mfumu zimene waona.” Pamenepo Mkusiyo anaweramira Yowabu ndi kuyamba kuthamanga.
21 Ndiyeno Yowabu anauza Mkusi+ kuti: “Pita ukauze mfumu zimene waona.” Pamenepo Mkusiyo anaweramira Yowabu ndi kuyamba kuthamanga.