Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Samueli 18:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Choncho mfumu inawauza kuti: “Ndichita zilizonse zimene inu mukuona kuti n’zabwino.”+ Pamenepo mfumu inangoima pambali pa chipata,+ ndipo anthu onse anapita kunkhondo m’magulu a anthu 100 ndi 1,000.+

  • 2 Samueli 18:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Tsopano Davide anali atakhala pakati pa zipata ziwiri.+ Pa nthawiyi mlonda+ anakwera padenga la mpanda kuchipata. Ndiyeno atakweza maso anaona munthu akuthamanga ali yekha.

  • 1 Mafumu 22:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Mfumu ya Isiraeli ndi Yehosafati mfumu ya Yuda anali atakhala pabwalo* la pachipata cha Samariya. Aliyense anakhala pampando wake wachifumu atavala zovala zachifumu.+ Pamaso pawo panali aneneri onse ndipo anali kuchita zinthu monga mmene aneneri amachitira.+

  • Yeremiya 38:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Tsopano Ebedi-meleki Mwitiyopiya,*+ amene anali nduna m’nyumba ya mfumu, ndipo pa nthawiyo anali m’nyumbamo, anamva kuti Yeremiya amuponya m’chitsime. Apa n’kuti mfumu itakhala pansi ku Chipata cha Benjamini.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena