Yeremiya 39:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Pita kwa Ebedi-meleki+ Mwitiyopiya ukamuuze kuti, ‘Yehova wa makamu, Mulungu wa Isiraeli, wanena kuti: “Taona! Ndikukwaniritsa mawu anga akuti mzinda uwu ndiugwetsera tsoka osati zinthu zabwino.+ Pa tsikulo zimene ndinanena zidzachitika iwe ukuona.”’+ Machitidwe 8:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Choncho, ananyamuka ndi kupita. Kumeneko anakumana ndi nduna+ ya ku Itiyopiya,+ munthu waulamuliro pansi pa Kandake, mfumukazi ya Itiyopiya. Iye anali woyang’anira chuma chonse cha mfumukaziyo. Iyeyu anapita ku Yerusalemu kukapembedza Mulungu,+
16 “Pita kwa Ebedi-meleki+ Mwitiyopiya ukamuuze kuti, ‘Yehova wa makamu, Mulungu wa Isiraeli, wanena kuti: “Taona! Ndikukwaniritsa mawu anga akuti mzinda uwu ndiugwetsera tsoka osati zinthu zabwino.+ Pa tsikulo zimene ndinanena zidzachitika iwe ukuona.”’+
27 Choncho, ananyamuka ndi kupita. Kumeneko anakumana ndi nduna+ ya ku Itiyopiya,+ munthu waulamuliro pansi pa Kandake, mfumukazi ya Itiyopiya. Iye anali woyang’anira chuma chonse cha mfumukaziyo. Iyeyu anapita ku Yerusalemu kukapembedza Mulungu,+