1 Mafumu 1:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 monga momwe ndinakulumbirira pa Yehova Mulungu wa Isiraeli, kuti, ‘Mwana wako Solomo adzakhala mfumu pambuyo panga ndipo iye ndi amene adzakhale pampando wanga wachifumu m’malo mwanga,’ ndi mmene ndichitire lero.”+
30 monga momwe ndinakulumbirira pa Yehova Mulungu wa Isiraeli, kuti, ‘Mwana wako Solomo adzakhala mfumu pambuyo panga ndipo iye ndi amene adzakhale pampando wanga wachifumu m’malo mwanga,’ ndi mmene ndichitire lero.”+