1 Mafumu 1:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pitani kwa Mfumu Davide mukanene kuti, ‘Kodi si inu mbuyanga mfumu amene munalumbirira ine kapolo wanu kuti: “Solomo mwana wako ndi amene adzakhale mfumu pambuyo panga, ndipo iye ndi amene adzakhale pampando wanga wachifumu”?+ Nanga n’chifukwa chiyani Adoniya wakhala mfumu?’ 1 Mafumu 1:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Bati-seba anayankha kuti: “Mbuyanga,+ ndinu amene munalumbira pa Yehova Mulungu wanu kwa ine kapolo wanu kuti, ‘Solomo mwana wako ndi amene adzakhale mfumu pambuyo pa ine, ndipo iye ndi amene adzakhale pampando wanga wachifumu.’+
13 Pitani kwa Mfumu Davide mukanene kuti, ‘Kodi si inu mbuyanga mfumu amene munalumbirira ine kapolo wanu kuti: “Solomo mwana wako ndi amene adzakhale mfumu pambuyo panga, ndipo iye ndi amene adzakhale pampando wanga wachifumu”?+ Nanga n’chifukwa chiyani Adoniya wakhala mfumu?’
17 Bati-seba anayankha kuti: “Mbuyanga,+ ndinu amene munalumbira pa Yehova Mulungu wanu kwa ine kapolo wanu kuti, ‘Solomo mwana wako ndi amene adzakhale mfumu pambuyo pa ine, ndipo iye ndi amene adzakhale pampando wanga wachifumu.’+