-
2 Mbiri 10:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Rehobowamu atamva zimenezi anauza anthuwo kuti: “Pitani kaye kwa masiku atatu, ndipo mukabwerenso kwa ine.” Anthuwo anapitadi.
-