Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 11:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 koma sindidzauchotsa wonse.+ Ndidzapereka fuko limodzi kwa mwana wako, chifukwa cha Davide mtumiki wanga+ ndiponso chifukwa cha Yerusalemu, mzinda umene ndausankha.”+

  • 2 Mbiri 10:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Koma Rehobowamu anapitiriza kulamulira ana a Isiraeli amene anali kukhala m’mizinda ya ku Yuda.+

  • 2 Mbiri 11:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Ansembe ndi Alevi m’madera awo onse mu Isiraeli yense, anakhala kumbali ya Rehobowamu.

  • 2 Mbiri 11:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Koma anthu a m’mafuko onse a Isiraeli amene anali ndi mtima wofunafuna Yehova Mulungu wa Isiraeli, anatsatira ansembe ku Yerusalemu+ kukapereka nsembe+ kwa Yehova Mulungu wa makolo awo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena