Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 6:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Asiriyawo atayamba kupita kumene kunali Elisa, iye anapemphera kwa Yehova kuti: “Chonde chititsani khungu mtundu uwu.” Chotero iye anawachititsa khungu+ malinga ndi mawu a Elisa.

  • Machitidwe 5:39
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 39 Koma ngati ikuchokera kwa Mulungu,+ simungathe kuwaletsa.+ Mukaumirira mukhoza kupezeka kuti mukulimbana ndi Mulungu.”+

  • Machitidwe 13:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Tsopano tamvera! Dzanja la Yehova lili pa iwe, ndipo ukhala wakhungu. Kwa kanthawi, suthanso kuona kuwala kwa dzuwa.” Nthawi yomweyo nkhungu yamphamvu ndi mdima wandiweyani zinamugwera, ndipo anafufuza uku ndi uku kufuna anthu oti amugwire dzanja ndi kumutsogolera.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena