1 Mafumu 20:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Choncho mneneriyo anauza mnzakeyo kuti: “Popeza sunamvere mawu a Yehova, ukachoka pano ukumana ndi mkango ndipo ukupha ndithu.” Kenako mnzakeyo anachoka ndipo mkango+ unamupeza n’kumupha.+ 2 Mafumu 17:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Atayamba kukhala mmenemo, iwo sanaope+ Yehova. Choncho Yehova anatumiza mikango+ pakati pawo ndipo inapha ena a iwo. Amosi 5:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 monga mmene zingakhalire kuti munthu pothawa mkango akukumana ndi chimbalangondo, ndipo pamene akulowa m’nyumba ndi kugwira khoma njoka ikumuluma.+
36 Choncho mneneriyo anauza mnzakeyo kuti: “Popeza sunamvere mawu a Yehova, ukachoka pano ukumana ndi mkango ndipo ukupha ndithu.” Kenako mnzakeyo anachoka ndipo mkango+ unamupeza n’kumupha.+
25 Atayamba kukhala mmenemo, iwo sanaope+ Yehova. Choncho Yehova anatumiza mikango+ pakati pawo ndipo inapha ena a iwo.
19 monga mmene zingakhalire kuti munthu pothawa mkango akukumana ndi chimbalangondo, ndipo pamene akulowa m’nyumba ndi kugwira khoma njoka ikumuluma.+