1 Mafumu 13:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Kenako mneneri wa ku Yudayo ananyamuka n’kumapita. Pambuyo pake mkango+ unam’peza panjira n’kumupha,+ ndipo mtembo wake unali pamsewu. Kumbali ina ya mtembowo kunaima bulu uja, ndipo mbali inayi kunaima mkangowo.
24 Kenako mneneri wa ku Yudayo ananyamuka n’kumapita. Pambuyo pake mkango+ unam’peza panjira n’kumupha,+ ndipo mtembo wake unali pamsewu. Kumbali ina ya mtembowo kunaima bulu uja, ndipo mbali inayi kunaima mkangowo.