1 Mafumu 13:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndiyeno anayamba kuuza munthu wa Mulungu woona yemwe anachokera ku Yuda uja, kuti: “Nazi zimene Yehova wanena, ‘Chifukwa chakuti wapandukira+ lamulo la Yehova, ndipo sunasunge lamulo limene Yehova Mulungu wako anakulamula,+ Miyambo 11:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Wolungamatu adzalandira mphoto yake padziko lapansi.+ Ndiye kuli bwanji woipa ndi wochimwa?+ Aheberi 12:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Pakuti Mulungu wathu alinso moto wowononga.+
21 Ndiyeno anayamba kuuza munthu wa Mulungu woona yemwe anachokera ku Yuda uja, kuti: “Nazi zimene Yehova wanena, ‘Chifukwa chakuti wapandukira+ lamulo la Yehova, ndipo sunasunge lamulo limene Yehova Mulungu wako anakulamula,+