1 Mafumu 15:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iye analamulira zaka zitatu ku Yerusalemu. Mayi ake dzina lawo linali Maaka,+ mdzukulu wa Abishalomu.*+ 2 Mbiri 11:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Pambuyo pake Rehobowamu anakwatira Maaka+ mdzukulu wa Abisalomu.+ Kenako mkaziyo anam’berekera ana awa: Abiya,+ Atai, Ziza ndi Selomiti. 2 Mbiri 13:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iye analamulira zaka zitatu ku Yerusalemu. Mayi ake dzina lawo linali Mikaya+ mwana wa Uriyeli wa ku Gibeya.+ Kenako pakati pa Abiya ndi Yerobowamu panachitika nkhondo.+
2 Iye analamulira zaka zitatu ku Yerusalemu. Mayi ake dzina lawo linali Maaka,+ mdzukulu wa Abishalomu.*+
20 Pambuyo pake Rehobowamu anakwatira Maaka+ mdzukulu wa Abisalomu.+ Kenako mkaziyo anam’berekera ana awa: Abiya,+ Atai, Ziza ndi Selomiti.
2 Iye analamulira zaka zitatu ku Yerusalemu. Mayi ake dzina lawo linali Mikaya+ mwana wa Uriyeli wa ku Gibeya.+ Kenako pakati pa Abiya ndi Yerobowamu panachitika nkhondo.+