1 Mafumu 15:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 M’chaka cha 18 cha Mfumu Yerobowamu+ mwana wa Nebati,+ Abiyamu anakhala mfumu ya Yuda.+ 2 Mbiri 12:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pomalizira pake, Rehobowamu anagona pamodzi ndi makolo ake+ ndipo anaikidwa m’manda mu Mzinda wa Davide.+ Kenako Abiya+ mwana wake anayamba kulamulira m’malo mwake. Mateyu 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Solomo anabereka Rehobowamu.+Rehobowamu anabereka Abiya.Abiya+ anabereka Asa.+
16 Pomalizira pake, Rehobowamu anagona pamodzi ndi makolo ake+ ndipo anaikidwa m’manda mu Mzinda wa Davide.+ Kenako Abiya+ mwana wake anayamba kulamulira m’malo mwake.