1 Mafumu 14:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Choncho Ahiya atangomva phokoso la mapazi a mkazi wa Yerobowamu pamene anali kulowa pakhomo, anayamba kulankhula kuti: “Lowa mkazi wa Yerobowamu.+ N’chifukwa chiyani ukudzisintha kuti usadziwike pamene ine ndatumidwa kwa iwe ndi uthenga wopweteka?
6 Choncho Ahiya atangomva phokoso la mapazi a mkazi wa Yerobowamu pamene anali kulowa pakhomo, anayamba kulankhula kuti: “Lowa mkazi wa Yerobowamu.+ N’chifukwa chiyani ukudzisintha kuti usadziwike pamene ine ndatumidwa kwa iwe ndi uthenga wopweteka?