Ekisodo 14:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndipo Aiguputo adzadziwa kuti ine ndine Yehova, ndikadzipezera ulemerero mwa kugonjetsa Farao, magaleta ake ankhondo ndi asilikali ake apamahatchi.”+ Salimo 37:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Pakuti anthu oipa adzatheratu onse,+Ndipo adani a Yehova adzafanana ndi busa la msipu wobiriwira mochititsa kaso.Iwo adzatha.+ Adzazimiririka ndi kusanduka utsi.+
18 Ndipo Aiguputo adzadziwa kuti ine ndine Yehova, ndikadzipezera ulemerero mwa kugonjetsa Farao, magaleta ake ankhondo ndi asilikali ake apamahatchi.”+
20 Pakuti anthu oipa adzatheratu onse,+Ndipo adani a Yehova adzafanana ndi busa la msipu wobiriwira mochititsa kaso.Iwo adzatha.+ Adzazimiririka ndi kusanduka utsi.+