Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 10:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Pomaliza pake, iwo anabwera kudzapereka nsembe zopsereza ndi nsembe zina. Yehu anaika amuna 80 panja oti amuthandize ndipo anawauza kuti: “Aliyense amene athawitse munthu pa anthu amene ndikuwapereka m’manja mwanu, moyo wake ulowa m’malo mwa munthuyo.”+

  • Machitidwe 12:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Herode+ anafunafuna Petulo pena paliponse, ndipo atalephera kumupeza, anapanikiza alondawo ndi mafunso ndi kulamula kuti awatenge, akawapatse chilango.+ Pamenepo Herode anachoka ku Yudeya ndi kupita ku Kaisareya, kumene anakhalako kanthawi ndithu.

  • Machitidwe 16:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Woyang’anira ndende uja atadzuka ku tulo take ndi kuona kuti zitseko za ndende n’zotseguka, anasolola lupanga lake kuti adziphe,+ poganiza kuti akaidiwo athawa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena