2 Mbiri 18:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Aneneri ena onse analinso kulosera zofanana ndi zomwezo, ndipo anali kunena kuti: “Pitani ku Ramoti-giliyadi ndipo mukapambana.+ Yehova akaperekadi mzindawo m’manja mwanu mfumu.”+
11 Aneneri ena onse analinso kulosera zofanana ndi zomwezo, ndipo anali kunena kuti: “Pitani ku Ramoti-giliyadi ndipo mukapambana.+ Yehova akaperekadi mzindawo m’manja mwanu mfumu.”+