1 Mafumu 22:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Aneneri ena onse analinso kulosera zofanana ndi zomwezo, ndipo anali kunena kuti: “Pitani ku Ramoti-giliyadi ndipo mukapambana. Yehova akaperekadi mzindawo m’manja mwanu mfumu.”+
12 Aneneri ena onse analinso kulosera zofanana ndi zomwezo, ndipo anali kunena kuti: “Pitani ku Ramoti-giliyadi ndipo mukapambana. Yehova akaperekadi mzindawo m’manja mwanu mfumu.”+