2 Samueli 8:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Davide anakhazikitsa midzi ya asilikali mu Edomu.+ Mu Edomu yense anaikamo midzi ya asilikali, moti Aedomu anakhala antchito a Davide+ ndipo Yehova anali kupulumutsa Davide kulikonse kumene anali kupita.+ 2 Mafumu 8:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 M’masiku a Yehoramu, Aedomu+ anagalukira Yuda. Iwo anachoka m’manja mwa Yuda n’kusankha mfumu+ yoti iziwalamulira. Salimo 108:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mowabu+ ndi beseni langa losambiramo.+Ndidzaponyera Edomu+ nsapato zanga.+Ndidzafuula mosangalala+ chifukwa chogonjetsa Filisitiya.”+
14 Davide anakhazikitsa midzi ya asilikali mu Edomu.+ Mu Edomu yense anaikamo midzi ya asilikali, moti Aedomu anakhala antchito a Davide+ ndipo Yehova anali kupulumutsa Davide kulikonse kumene anali kupita.+
20 M’masiku a Yehoramu, Aedomu+ anagalukira Yuda. Iwo anachoka m’manja mwa Yuda n’kusankha mfumu+ yoti iziwalamulira.
9 Mowabu+ ndi beseni langa losambiramo.+Ndidzaponyera Edomu+ nsapato zanga.+Ndidzafuula mosangalala+ chifukwa chogonjetsa Filisitiya.”+