Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 27:40
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 40 Udzakhalira moyo lupanga+ ndipo udzatumikira m’bale wako.+ Koma ukadzatopa ndi goli lake, udzalithyola ndi kulichotsa m’khosi mwako.”+

  • 2 Samueli 8:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Davide anakhazikitsa midzi ya asilikali mu Edomu.+ Mu Edomu yense anaikamo midzi ya asilikali, moti Aedomu anakhala antchito a Davide+ ndipo Yehova anali kupulumutsa Davide kulikonse kumene anali kupita.+

  • 2 Mafumu 3:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Choncho mfumu ya Isiraeli, mfumu ya Yuda, ndi mfumu ya Edomu+ ananyamuka n’kuyenda mozungulira kwa masiku 7. Koma kuchipululuko kunalibe madzi oti anthuwo amwe pamodzi ndi ziweto zimene anali kuyenda nazo.

  • 2 Mbiri 21:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 M’masiku a Yehoramu, Aedomu+ anagalukira Yuda.+ Iwo anachoka m’manja mwa Yuda n’kusankha mfumu yoti iziwalamulira.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena