-
2 Samueli 13:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Atatero, Yehonadabu anamuuza kuti: “Ugone pabedi lako ndi kunamizira kudwala.+ Mosakayikira bambo ako adzabwera kudzakuona, ndipo udzawauze kuti, ‘Chonde lolani kuti mlongo wanga Tamara abwere adzandipatse chakudya monga munthu wodwala. Ndikufuna kuti andipangire chakudya chonditonthoza pamaso panga, ine ndikuona, ndipo ndidye kuchokera m’manja mwake.’”+
-