Genesis 31:54 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 54 Pambuyo pake, Yakobo anapereka nsembe m’phirimo n’kuitana abale ake kuti adye chakudya.+ Motero iwo anadya chakudya n’kugona m’phirimo usiku umenewo. Esitere 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 M’chaka chachitatu cha ulamuliro wake, Ahasiwero anakonzera phwando+ akalonga ndi atumiki ake onse, akuluakulu a asilikali a Perisiya+ ndi Mediya,+ anthu olemekezeka+ ndi akalonga a m’zigawo za ufumu wake.+ Danieli 5:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndiyeno mfumu Belisazara+ anakonzera nduna zake 1,000 phwando lalikulu, ndipo iyeyo anali kumwa vinyo+ atakhala kutsogolo kwawo.
54 Pambuyo pake, Yakobo anapereka nsembe m’phirimo n’kuitana abale ake kuti adye chakudya.+ Motero iwo anadya chakudya n’kugona m’phirimo usiku umenewo.
3 M’chaka chachitatu cha ulamuliro wake, Ahasiwero anakonzera phwando+ akalonga ndi atumiki ake onse, akuluakulu a asilikali a Perisiya+ ndi Mediya,+ anthu olemekezeka+ ndi akalonga a m’zigawo za ufumu wake.+
5 Ndiyeno mfumu Belisazara+ anakonzera nduna zake 1,000 phwando lalikulu, ndipo iyeyo anali kumwa vinyo+ atakhala kutsogolo kwawo.