Deuteronomo 14:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 mbawala yamphongo, insa, ngondo,+ mbuzi yakuthengo, mphalapala, nkhosa yakuthengo ndi chinkhoma. Maliro 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ulemerero+ wonse wamuchokera mwana wamkazi wa Ziyoni.Akalonga ake akhala ngati mbawala zamphongo zimene zikusowa msipu.+Iwo akuyenda mofooka+ pamaso pa wowazunza.*
6 Ulemerero+ wonse wamuchokera mwana wamkazi wa Ziyoni.Akalonga ake akhala ngati mbawala zamphongo zimene zikusowa msipu.+Iwo akuyenda mofooka+ pamaso pa wowazunza.*