2 Samueli 12:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndiyeno Davide anayamba kutonthoza mkazi wake Bati-seba.+ Kuwonjezera apo, analowa kwa iye ndipo anagona naye. Patapita nthawi, anamuberekera mwana wamwamuna+ amene anamutcha dzina lakuti Solomo.*+ Yehova anam’konda mwana ameneyu.+ 1 Mafumu 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Zitatero, Bati-seba analowa kuchipinda kumene kunali mfumu.+ Mfumuyo inali yokalamba+ kwambiri ndipo Abisagi+ Msunemu anali kuisamalira.
24 Ndiyeno Davide anayamba kutonthoza mkazi wake Bati-seba.+ Kuwonjezera apo, analowa kwa iye ndipo anagona naye. Patapita nthawi, anamuberekera mwana wamwamuna+ amene anamutcha dzina lakuti Solomo.*+ Yehova anam’konda mwana ameneyu.+
15 Zitatero, Bati-seba analowa kuchipinda kumene kunali mfumu.+ Mfumuyo inali yokalamba+ kwambiri ndipo Abisagi+ Msunemu anali kuisamalira.