2 Samueli 7:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 “Tsopano inu Yehova Mulungu, chitani mpaka kalekale mawu amene mwalankhula okhudza mtumiki wanu ndi nyumba yake. Chitani mmene mwanenera.+ 1 Mbiri 17:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndidzamukhazikitsa iye kukhala woyang’anira nyumba yanga+ ndi ufumu wanga+ mpaka kalekale, ndipo mpando wake wachifumu+ sudzatha mpaka kalekale.”’” 2 Mbiri 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Tsopano inu Yehova Mulungu, kwaniritsani+ lonjezo limene munapereka kwa Davide bambo anga. Pakuti ndinu amene mwandiika kukhala mfumu+ ya anthuwa amene ndi ochuluka kwambiri ngati fumbi lapadziko lapansi.+ Salimo 119:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Kumbukirani mawu amene munandiuza ine mtumiki wanu,+Mawu amene ndikuwayembekezera malinga ndi lonjezo lanu.+
25 “Tsopano inu Yehova Mulungu, chitani mpaka kalekale mawu amene mwalankhula okhudza mtumiki wanu ndi nyumba yake. Chitani mmene mwanenera.+
14 Ndidzamukhazikitsa iye kukhala woyang’anira nyumba yanga+ ndi ufumu wanga+ mpaka kalekale, ndipo mpando wake wachifumu+ sudzatha mpaka kalekale.”’”
9 Tsopano inu Yehova Mulungu, kwaniritsani+ lonjezo limene munapereka kwa Davide bambo anga. Pakuti ndinu amene mwandiika kukhala mfumu+ ya anthuwa amene ndi ochuluka kwambiri ngati fumbi lapadziko lapansi.+
49 Kumbukirani mawu amene munandiuza ine mtumiki wanu,+Mawu amene ndikuwayembekezera malinga ndi lonjezo lanu.+