Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Samueli 7:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Masiku ako akadzakwana,+ ndipo ukadzagona pamodzi ndi makolo ako,+ pamenepo ndidzautsa mbewu yako yobwera pambuyo pako, imene idzatuluka m’chiuno mwako. Ndipo ndidzakhazikitsadi ufumu wake.+

  • 1 Mbiri 17:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Pakuti inu Mulungu wanga mwandiululira ine mtumiki wanu cholinga chanu chondimangira nyumba,+ n’chifukwa chake ine mtumiki wanu ndapeza nthawi yopemphera pamaso panu.

  • 1 Mbiri 28:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 “Kuwonjezera pamenepo, anandiuza kuti: ‘Mwana wako Solomo ndiye adzamanga nyumba yanga+ ndiponso mabwalo anga, chifukwa ndam’sankha kuti akhale mwana wanga+ ndipo ine ndidzakhala atate wake.+

  • Salimo 132:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Yehova walumbira kwa Davide,+

      Ndithudi sadzabweza mawu ake akuti:+

      “Ndidzaika pampando wako wachifumu+

      Chipatso cha mimba yako.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena