1 Mafumu 20:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndiyeno mneneri wina anapita kwa Ahabu mfumu ya Isiraeli,+ n’kumuuza kuti: “Yehova wanena kuti,+ ‘Kodi waona khamu lalikulu lonseli? Ndilipereka m’manja mwako lero, ndipo udziwadi kuti ine ndine Yehova.’”+
13 Ndiyeno mneneri wina anapita kwa Ahabu mfumu ya Isiraeli,+ n’kumuuza kuti: “Yehova wanena kuti,+ ‘Kodi waona khamu lalikulu lonseli? Ndilipereka m’manja mwako lero, ndipo udziwadi kuti ine ndine Yehova.’”+