1 Mbiri 29:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kenako Davide anatamanda+ Yehova pamaso pa mpingo wonse,+ kuti: “Mudalitsike+ inu Yehova Mulungu wa Isiraeli+ atate wathu, kuyambira kalekale mpaka kalekale. 2 Mbiri 20:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Pa tsiku lachinayi anasonkhana pachigwa cha Beraka ndipo kumeneko anatamanda Yehova.+ N’chifukwa chake malowo anawatcha dzina+ lakuti chigwa cha Beraka* mpaka lero. Salimo 41:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Adalitsike Yehova Mulungu wa Isiraeli,+Kuyambira kalekale mpaka kalekale.+Ame! Ame!*+
10 Kenako Davide anatamanda+ Yehova pamaso pa mpingo wonse,+ kuti: “Mudalitsike+ inu Yehova Mulungu wa Isiraeli+ atate wathu, kuyambira kalekale mpaka kalekale.
26 Pa tsiku lachinayi anasonkhana pachigwa cha Beraka ndipo kumeneko anatamanda Yehova.+ N’chifukwa chake malowo anawatcha dzina+ lakuti chigwa cha Beraka* mpaka lero.