Salimo 102:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 102 Inu Yehova, imvani pemphero langa.+Imvani kufuula kwanga kopempha thandizo.+ Salimo 141:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pemphero langa likhale lokonzedwa ngati zofukiza+ pamaso panu,+Mapembedzero anga akhale ngati nsembe yambewu yamadzulo.+
2 Pemphero langa likhale lokonzedwa ngati zofukiza+ pamaso panu,+Mapembedzero anga akhale ngati nsembe yambewu yamadzulo.+