Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 29:39
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 39 Uzipereka mwana wa nkhosa mmodzi m’mawa,+ ndipo mwana wa nkhosa winayo madzulo kuli kachisisira.*+

  • Salimo 28:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Imvani mawu anga ochonderera pamene ndikufuulira inu kuti mundithandize,

      Pamene ndikukweza manja anga,+ nditayang’ana kumene kuli chipinda chamkati cha m’malo anu opatulika.+

  • Salimo 63:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Choncho ndidzakutamandani pa nthawi yonse ya moyo wanga.+

      Ndidzapemphera m’dzina lanu nditakweza manja anga.+

  • Salimo 134:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Pamene mukupemphera mutakweza manja anu, muzikhala oyera,+

      Ndipo tamandani Yehova.+

  • 1 Timoteyo 2:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Choncho, ndikufuna kuti kulikonse amuna apitirize kupemphera, kukweza m’mwamba manja awo oyera+ popanda kukwiyirana+ ndi kutsutsana.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena