Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 10:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Ofiri,+ Havila+ ndi Yobabi.+ Onsewa anali ana a Yokitani.

  • 1 Mafumu 10:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Zombo+ za Hiramu zimene zinabweretsa golide kuchokera ku Ofiri,+ zinabweretsanso matabwa a mtengo wa m’bawa+ ochuluka zedi ndi miyala yamtengo wapatali.+

  • 1 Mbiri 29:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Chumacho chili motere: Matalente* 3,000 a golide wa ku Ofiri,+ matalente 7,000 a siliva woyengedwa bwino wokutira makoma a nyumbazo,

  • 2 Mbiri 9:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Kuwonjezera pamenepo, atumiki a Hiramu+ ndi atumiki a Solomo amene anabwera ndi golide+ kuchokera ku Ofiri, anabweretsanso matabwa a mtengo wa m’bawa+ ndi miyala yamtengo wapatali.+

  • Yobu 22:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Ndipo ukataya golide wako wamtengo wapatali m’fumbi,

      Ukataya golide wa ku Ofiri+ m’miyala ya m’zigwa,*

  • Salimo 45:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Ana aakazi+ a mafumu ali m’gulu la akazi ako okondedwa.

      Mkazi wamkulu wa mfumu+ waima kudzanja lako lamanja atavala zovala zagolide wa ku Ofiri.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena