1 Mafumu 9:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Iwo ankapita ku Ofiri+ n’kukatenga golide wokwana matalente 420,+ n’kubwera naye kwa Mfumu Solomo. Yobu 28:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Sangazigule ndi golide wa ku Ofiri,+Kapena mwala wosowa wa onekisi ndi wa safiro. Salimo 45:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ana aakazi+ a mafumu ali m’gulu la akazi ako okondedwa.Mkazi wamkulu wa mfumu+ waima kudzanja lako lamanja atavala zovala zagolide wa ku Ofiri.+ Yesaya 13:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndidzachititsa kuti anthu azisowa kwambiri kuposa golide woyengedwa bwino,+ ndiponso ndidzachititsa kuti anthu ochokera kufumbi azisowa kwambiri kuposa golide wa ku Ofiri.+
28 Iwo ankapita ku Ofiri+ n’kukatenga golide wokwana matalente 420,+ n’kubwera naye kwa Mfumu Solomo.
9 Ana aakazi+ a mafumu ali m’gulu la akazi ako okondedwa.Mkazi wamkulu wa mfumu+ waima kudzanja lako lamanja atavala zovala zagolide wa ku Ofiri.+
12 Ndidzachititsa kuti anthu azisowa kwambiri kuposa golide woyengedwa bwino,+ ndiponso ndidzachititsa kuti anthu ochokera kufumbi azisowa kwambiri kuposa golide wa ku Ofiri.+