-
2 Mafumu 8:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Choncho Hazaeli anatenga mphatsozo n’kupita kukakumana naye. Anatenga chinthu chilichonse chabwino cha m’Damasiko. Mphatsozo anazinyamula pangamira zokwana 40. Atafika, anaima pamaso pa Elisa n’kunena kuti: “Mwana wanu+ Beni-hadadi mfumu ya Siriya wandituma kudzakufunsani kuti, ‘Kodi ndichira matenda angawa?’”
-