1 Mbiri 15:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Chifukwa chakuti ulendo woyamba uja inuyo simunapite kukalitenga,+ mkwiyo wa Yehova Mulungu wathu unatiphulikira,+ pakuti sitinatsatire malangizo ake monga mwa mwambo wathu.”+ Salimo 78:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Nthawi zonse akayamba kuwapha, iwo anali kumufunafuna.+Anali kutembenuka ndi kuyamba kufunafuna Mulungu.+ Miyambo 19:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kupusa kwa munthu wochokera kufumbi n’kumene kumapotoza njira yake,+ choncho mtima wake umakwiyira Yehova.+ Yesaya 8:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Aliyense adzadutsa m’dzikolo akuzunzika ndiponso ali ndi njala.+ Chifukwa chakuti ali ndi njala ndiponso wakwiya, adzatukwana mfumu yake ndi Mulungu+ wake ndipo azidzayang’ana kumwamba.
13 Chifukwa chakuti ulendo woyamba uja inuyo simunapite kukalitenga,+ mkwiyo wa Yehova Mulungu wathu unatiphulikira,+ pakuti sitinatsatire malangizo ake monga mwa mwambo wathu.”+
34 Nthawi zonse akayamba kuwapha, iwo anali kumufunafuna.+Anali kutembenuka ndi kuyamba kufunafuna Mulungu.+
3 Kupusa kwa munthu wochokera kufumbi n’kumene kumapotoza njira yake,+ choncho mtima wake umakwiyira Yehova.+
21 Aliyense adzadutsa m’dzikolo akuzunzika ndiponso ali ndi njala.+ Chifukwa chakuti ali ndi njala ndiponso wakwiya, adzatukwana mfumu yake ndi Mulungu+ wake ndipo azidzayang’ana kumwamba.