Yesaya 36:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Musamvere Hezekiya chifukwa mfumu ya Asuri yanena kuti: “Ndigonjereni,+ ndipo bwerani kwa ine. Aliyense azidya zochokera mumtengo wake wa mpesa ndi mumtengo wake wa mkuyu,+ komanso aliyense azimwa madzi a m’chitsime chake,+
16 Musamvere Hezekiya chifukwa mfumu ya Asuri yanena kuti: “Ndigonjereni,+ ndipo bwerani kwa ine. Aliyense azidya zochokera mumtengo wake wa mpesa ndi mumtengo wake wa mkuyu,+ komanso aliyense azimwa madzi a m’chitsime chake,+