2 Mafumu 19:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiika maganizo mwa iye,+ kuti akamva nkhani inayake,+ abwerere kudziko lake. Ndipo mosalephera ndidzachititsa kuti akaphedwe ndi lupanga m’dziko lake.”’”+ 2 Mafumu 19:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Chifukwa kundipsera mtima kwako+ ndi kufuula kwako zafika m’makutu mwanga,+Ndithu ndidzakola mphuno yako ndi ngowe yanga, ndipo ndidzamanga zingwe zanga pakamwa pako.+Kenako ndidzakukoka n’kukubweza kudzera njira imene unadutsa pobwera.”+
7 Ndiika maganizo mwa iye,+ kuti akamva nkhani inayake,+ abwerere kudziko lake. Ndipo mosalephera ndidzachititsa kuti akaphedwe ndi lupanga m’dziko lake.”’”+
28 Chifukwa kundipsera mtima kwako+ ndi kufuula kwako zafika m’makutu mwanga,+Ndithu ndidzakola mphuno yako ndi ngowe yanga, ndipo ndidzamanga zingwe zanga pakamwa pako.+Kenako ndidzakukoka n’kukubweza kudzera njira imene unadutsa pobwera.”+