2 Mafumu 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Choncho mfumu ya Isiraeli, mfumu ya Yuda, ndi mfumu ya Edomu+ ananyamuka n’kuyenda mozungulira kwa masiku 7. Koma kuchipululuko kunalibe madzi oti anthuwo amwe pamodzi ndi ziweto zimene anali kuyenda nazo.
9 Choncho mfumu ya Isiraeli, mfumu ya Yuda, ndi mfumu ya Edomu+ ananyamuka n’kuyenda mozungulira kwa masiku 7. Koma kuchipululuko kunalibe madzi oti anthuwo amwe pamodzi ndi ziweto zimene anali kuyenda nazo.