Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Samueli 8:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Davide anakhazikitsa midzi ya asilikali mu Edomu.+ Mu Edomu yense anaikamo midzi ya asilikali, moti Aedomu anakhala antchito a Davide+ ndipo Yehova anali kupulumutsa Davide kulikonse kumene anali kupita.+

  • 1 Mafumu 22:47
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 47 Pa nthawi imeneyo ku Edomu+ kunalibe mfumu. Nduna ndi imene inali kulamulira monga mfumu.+

  • Mlaliki 4:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Ngati wina angagonjetse munthu mmodzi, anthu awiri akhoza kulimbana naye.+ Ndipo chingwe chopotedwa ndi zingwe zitatu sichingaduke msanga.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena