1 Samueli 2:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Ndiyeno aliyense wotsala+ m’nyumba yako adzafika ndi kumugwadira kuti alandire ndalama za malipiro ndi mtanda wobulungira wa mkate, ndipo adzati: “Ndiloleni chonde ndigwire ntchito monga wansembe kuti ndipezeko kachakudya.”’”+ Ezekieli 44:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Iwowa ndi amene azidzadya nsembe yambewu, nsembe yamachimo ndi nsembe ya kupalamula.+ Chilichonse choperekedwa kwa Mulungu mu Isiraeli chidzakhala chawo.+
36 Ndiyeno aliyense wotsala+ m’nyumba yako adzafika ndi kumugwadira kuti alandire ndalama za malipiro ndi mtanda wobulungira wa mkate, ndipo adzati: “Ndiloleni chonde ndigwire ntchito monga wansembe kuti ndipezeko kachakudya.”’”+
29 Iwowa ndi amene azidzadya nsembe yambewu, nsembe yamachimo ndi nsembe ya kupalamula.+ Chilichonse choperekedwa kwa Mulungu mu Isiraeli chidzakhala chawo.+