1 Samueli 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pamenepo Hana anaimirira atadya ndi kumwa ku Silo. Apa n’kuti Eli wansembe atakhala pampando, pakhomo la kachisi+ wa Yehova. Nehemiya 10:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Wansembe, mwana wamwamuna wa Aroni, azikhala ndi Alevi pamene iwo akulandira chakhumi.* Aleviwo azipereka gawo limodzi mwa magawo 10 a chakhumicho kunyumba ya Mulungu+ wathu kuzipinda zodyera+ m’nyumba yosungiramo zinthu. Yeremiya 35:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Pita kunyumba ya Arekabu,+ ndipo ukalankhule nawo ndi kubwera nawo kunyumba ya Yehova. Ukalowe nawo m’chimodzi mwa zipinda zodyera ndipo ukawapatse vinyo kuti amwe.”
9 Pamenepo Hana anaimirira atadya ndi kumwa ku Silo. Apa n’kuti Eli wansembe atakhala pampando, pakhomo la kachisi+ wa Yehova.
38 Wansembe, mwana wamwamuna wa Aroni, azikhala ndi Alevi pamene iwo akulandira chakhumi.* Aleviwo azipereka gawo limodzi mwa magawo 10 a chakhumicho kunyumba ya Mulungu+ wathu kuzipinda zodyera+ m’nyumba yosungiramo zinthu.
2 “Pita kunyumba ya Arekabu,+ ndipo ukalankhule nawo ndi kubwera nawo kunyumba ya Yehova. Ukalowe nawo m’chimodzi mwa zipinda zodyera ndipo ukawapatse vinyo kuti amwe.”