2 Mbiri 35:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Atumiki akewo anamutsitsa m’galetalo n’kumukweza m’galeta lake lachiwiri lankhondo, n’kupita naye ku Yerusalemu.+ Choncho iye anafa+ ndipo anamuika m’manda a makolo ake.+ Ayuda onse ndi anthu onse okhala ku Yerusalemu anamulira+ Yosiya.
24 Atumiki akewo anamutsitsa m’galetalo n’kumukweza m’galeta lake lachiwiri lankhondo, n’kupita naye ku Yerusalemu.+ Choncho iye anafa+ ndipo anamuika m’manda a makolo ake.+ Ayuda onse ndi anthu onse okhala ku Yerusalemu anamulira+ Yosiya.