Yeremiya 26:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndiyeno Mfumu Yehoyakimu,+ asilikali ake onse amphamvu ndi akalonga onse anamva mawu amene Uliya anali kunena. Pamenepo mfumu inakonza zoti imuphe.+ Uliya atamva zimenezo, nthawi yomweyo anachita mantha+ ndipo anathawira ku Iguputo. Yeremiya 36:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Iwo sanachite mantha+ ndipo mfumu ndi atumiki ake onse amene anali kumvetsera mawu amenewa sanang’ambe zovala zawo.+
21 Ndiyeno Mfumu Yehoyakimu,+ asilikali ake onse amphamvu ndi akalonga onse anamva mawu amene Uliya anali kunena. Pamenepo mfumu inakonza zoti imuphe.+ Uliya atamva zimenezo, nthawi yomweyo anachita mantha+ ndipo anathawira ku Iguputo.
24 Iwo sanachite mantha+ ndipo mfumu ndi atumiki ake onse amene anali kumvetsera mawu amenewa sanang’ambe zovala zawo.+