Yesaya 26:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Inu Yehova, dzanja lanu lakwezeka,+ koma iwo sakuliona.+ Iwo adzaona mmene mukudziperekera kwa anthu anu, ndipo adzachita manyazi.+ Ndithu, moto+ wanu udzanyeketsa adani anu.
11 Inu Yehova, dzanja lanu lakwezeka,+ koma iwo sakuliona.+ Iwo adzaona mmene mukudziperekera kwa anthu anu, ndipo adzachita manyazi.+ Ndithu, moto+ wanu udzanyeketsa adani anu.