Genesis 45:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Aliyense wa iwo anam’patsa chovala choti asinthire,+ koma Benjamini anam’patsa zovala zosinthira zisanu, ndi ndalama zasiliva 300.+ Oweruza 14:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kenako Samisoni anawauza kuti: “Ndiloleni ndikuphereni mwambi.+ Ngati mundiuza tanthauzo lake, m’masiku 7+ a phwandoli, ndidzakupatsani malaya 30 amkati ndi zovala zina 30.+
22 Aliyense wa iwo anam’patsa chovala choti asinthire,+ koma Benjamini anam’patsa zovala zosinthira zisanu, ndi ndalama zasiliva 300.+
12 Kenako Samisoni anawauza kuti: “Ndiloleni ndikuphereni mwambi.+ Ngati mundiuza tanthauzo lake, m’masiku 7+ a phwandoli, ndidzakupatsani malaya 30 amkati ndi zovala zina 30.+