Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 49:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Ndidzatchera khutu kuti ndimvetsere mwambi.+

      Poimba zeze ndidzamasulira mawu anga ophiphiritsa.+

  • Salimo 78:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Ndidzatsegula pakamwa panga ndi kunena mwambi.+

      Ndidzanena mawu ophiphiritsa akalekale,+

  • Miyambo 1:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 kuti azitha kumvetsa mwambi ndi mawu ozunguza mutu,+ mawu a anthu anzeru+ ndi mikuluwiko yawo.+

  • Ezekieli 17:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 “Iwe mwana wa munthu, phera nyumba ya Isiraeli mwambi+ ndipo uwauze mawu ophiphiritsa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena