2 Mafumu 5:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndiyeno mfumu ya Siriya inauza Namani kuti: “Nyamuka, ndikupatsa kalata upite kwa mfumu ya Isiraeli.” Choncho iye ananyamuka atatenga+ matalente* 10 a siliva, masekeli 6,000 a golide,+ ndi zovala 10.+
5 Ndiyeno mfumu ya Siriya inauza Namani kuti: “Nyamuka, ndikupatsa kalata upite kwa mfumu ya Isiraeli.” Choncho iye ananyamuka atatenga+ matalente* 10 a siliva, masekeli 6,000 a golide,+ ndi zovala 10.+