1 Mafumu 14:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Nkhani zina zokhudza Rehobowamu ndi zonse zimene anachita, zinalembedwa m’buku+ la zochitika za m’nthawi ya mafumu a Yuda. 1 Mafumu 15:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Nkhani zina zonse zokhudza Asa, ndi zochita zake zonse zamphamvu, ndiponso zonse zimene anachita, ndi mizinda imene anamanga, zinalembedwa m’buku+ la zochitika za m’masiku a mafumu a Yuda. Koma mu ukalamba wake,+ mapazi ake anachita matenda.+ 2 Mafumu 15:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Nkhani zina zokhudza Azariya ndi zonse zimene anachita, zinalembedwa m’buku+ la zochitika za m’masiku a mafumu a Yuda. 2 Mafumu 15:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Nkhani zina zokhudza Yotamu ndi zimene anachita, zinalembedwa m’buku la zochitika za m’masiku a mafumu a Yuda.+
29 Nkhani zina zokhudza Rehobowamu ndi zonse zimene anachita, zinalembedwa m’buku+ la zochitika za m’nthawi ya mafumu a Yuda.
23 Nkhani zina zonse zokhudza Asa, ndi zochita zake zonse zamphamvu, ndiponso zonse zimene anachita, ndi mizinda imene anamanga, zinalembedwa m’buku+ la zochitika za m’masiku a mafumu a Yuda. Koma mu ukalamba wake,+ mapazi ake anachita matenda.+
6 Nkhani zina zokhudza Azariya ndi zonse zimene anachita, zinalembedwa m’buku+ la zochitika za m’masiku a mafumu a Yuda.
36 Nkhani zina zokhudza Yotamu ndi zimene anachita, zinalembedwa m’buku la zochitika za m’masiku a mafumu a Yuda.+