-
Numeri 18:28Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
28 Mwa njira imeneyi, inunso muzipereka chopereka chanu kwa Yehova. Muzipereka kuchokera pazakhumi zonse zimene muzilandira kuchokera kwa ana a Isiraeli. Kuchokera pazakhumizo, muzipereka chopereka chanu kwa Yehova mwa kupatsa wansembe Aroni.
-