2 Mafumu 14:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Yehova anali ataona mavuto aakulu omwe Aisiraeli anali kukumana nawo.+ Kunalibe ngakhale anthu onyozeka ndi opanda pake, ngakhalenso munthu aliyense woti akanathandiza Aisiraeli.+
26 Yehova anali ataona mavuto aakulu omwe Aisiraeli anali kukumana nawo.+ Kunalibe ngakhale anthu onyozeka ndi opanda pake, ngakhalenso munthu aliyense woti akanathandiza Aisiraeli.+