2 Mafumu 14:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Amaziya anapha Aedomu+ okwana 10,000 m’chigwa cha Mchere+ n’kulanda mzinda wa Sela pankhondo. Kenako mzindawo anayamba kuutcha Yokiteeli ndipo dzina lake ndi lomweli mpaka lero.
7 Amaziya anapha Aedomu+ okwana 10,000 m’chigwa cha Mchere+ n’kulanda mzinda wa Sela pankhondo. Kenako mzindawo anayamba kuutcha Yokiteeli ndipo dzina lake ndi lomweli mpaka lero.